CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Mumaphunzirapo Kanthu Mukalakwitsa Zinazake?
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Mafumu.]
Adoniya anasonyezedwa chifundo atachita zinthu modzikweza pofuna kuti akhale mfumu (1Mf 1:5, 52, 53; it-2 987 ¶4)
Adoniya sanaphunzirepo kanthu pa zimene analakwitsa ndipo anakumana ndi mavuto (1Mf 2:15-17, 22, 23; it-1 49)
Munthu wanzeru amaphunzirapo kanthu akalakwitsa zinazake. Komanso kuwonjezera pamenepo amaphunziranso kanthu pa zimene ena alakwitsa.—1Ak 10:11.