August 22-28
1 MAFUMU 7
Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zipilala Ziwiri”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 7:23—Kodi tikuphunzira chiyani pa “thanki yamkuwa” yaikulu imene inamangidwa pakachisi? (it-1 263)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 7:1-12 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 06 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (5 min.)
“Ntchito Yapadera Yoyambitsa Maphunziro a Baibulo mu September”: (10 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Phunziro la Baibulo—Sl 37:29. Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza zokhudza ntchito yapaderayi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 17
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero