July 25-31
2 SAMUELI 23-24
Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mumapereka Nsembe?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 23:15-17—N’chifukwa chiyani Davide anakana kumwa madzi? (w05 5/15 19 ¶6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 23:1-12 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani kukambirana pogwiritsa ntchito tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. Konzani zoti mudzabwerenso kuti mudzakambirane phunziro 01 n’kupeza yankho la funso lake. (th phunziro 9)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pitani kwa munthu amene analandira kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 05 zomwe taphunzira, kubwereza, komanso zolinga (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Muzipereka Nsembe Mofunitsitsa (Sl 54:6): (9 min.) Onerani vidiyoyi.
Khalani Bwenzi la Yehova—Kudzimana: (6 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: Kodi Kalebe ndi Sofiya anadzimana chiyani? Kodi chitsanzo cha Yesu chinathandiza bwanji Kalebe? Kodi inuyo mwadzimana zinthu ziti chifukwa cha Yehova komanso anthu ena?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 13 ndi mawu akumapeto 1
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero