July 4-10
2 SAMUELI 18-19
Nyimbo Na. 138 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Barizilai Anali Wodzichepetsa”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 19:24-30—Kodi chitsanzo cha Mefiboseti chingatithandize bwanji? (w20.04 30 ¶19)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 19:31-43 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Cholinga cha Mulungu—Ge 1:28. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. a Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)
Nkhani: (5 min.) w21.08 23-25 ¶15-19—Mutu: Kodi ndi Zolinga Ziti Zimene Tingakhale Nazo Ngati Zinthu pa Moyo Wathu Sizikutilola Kuchita Zambiri? (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi—Upainiya”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Molimba Mtima—Apainiya.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 11
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero