Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

August 14-20

NEHEMIYA 8-9

August 14-20

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ne 8:2, 8​—Ngati anthu omwe anasonkhana “akanatha kumvetsera ndi kuzindikira” pamene Chilamulo chinkawerengedwa, n’chifukwa chiyani Alevi ankafunika kuchifotokozera? (it-1 145 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 8:1-12 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU