Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova

Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova

Mabanja anapemphedwa kuti asiye nyumba komanso malo awo n’kupita ku Yerusalemu (Ne 11:1; w98 10/15 22 ¶13)

Anthu omwe anasiya zinthu zimenezi anadalitsidwa (Ne 11:2; w86 2/15 31)

Nthawi zonse madalitso ochokera kwa Yehova amakhala ochuluka kwambiri kuposa zinthu zimene tingasiye (Mki 3:10; w16.04 8 ¶15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndapeza madalitso otani chifukwa cha zinthu zomwe ndinasiya pofuna kutumikira Yehova?’