August 28–September 3
NEHEMIYA 12-13
Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova Mukamasankha Anthu Ocheza Nawo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Ne 13:10—Oimba a pakachisi anali Alevi, ndiye n’chifukwa chiyani anatchulidwa mosiyana? (it-2 452 ¶9)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 12:27-39 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 16)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 11 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (5 min.)
“Tsanzirani Chikondi Chokhulupirika cha Yehova”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 55 mfundo 5, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero