August 7-13
NEHEMIYA 5-7
Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Ne 6:13—N’chifukwa chiyani likanakhala tchimo Nehemiya akanati akabisale m’kachisi? (w07 7/1 30 ¶15)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 5:1-13 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 9)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 6)
Nkhani: (5 min.) w13 5/15 7 ¶17-19—Mutu: Alaliki Abwino Amathandizana. (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Amachita Khama Kuti Atitumikire”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 53
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero