Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa

Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa

Nehemiya sanagwiritse ntchito udindo wake kuti adzipindulitse yekha (Ne 5:14, 15, 17, 18; w02 11/1 27 ¶3)

Sikuti Nehemiya ankangoyang’anira, koma ankagwiranso nawo ntchitoyo (Ne 5:16; w16.09 6 ¶16)

Nehemiya anapempha Yehova kuti amukumbukire chifukwa cha kudzipereka komanso chikondi chimene anasonyeza (Ne 5:19; w00 2/1 32)

Ngakhale kuti Nehemiya anali bwanamkubwa, sankayembekezera kuti azilandira ulemu wapadera. Iye ndi chitsanzo chabwino kwa anthu amene ali ndi mwayi wa utumiki wapadera komanso maudindo mu mpingo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimakhala wofunitsitsa kuchitira ena zinthu, kapena ndimangofuna kuti anthu azindichitira ineyo zinazake?’