Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zochita za Ezara Zinachititsa Kuti Dzina la Yehova Lilemekezedwe

Zochita za Ezara Zinachititsa Kuti Dzina la Yehova Lilemekezedwe

Ezara analola kuti mawu a Mulungu azimufika pamtima ndipo zimenezi zinakhudza zochita zake (Eza 7:10; w00 10/1 14 ¶8)

Ezara anathandiza anthu ena kuzindikira nzeru za Mulungu (Eza 7:25; si 75 ¶5)

Chifukwa chakuti anadzichepetsa pamaso pa Mulungu, Ezara anali wotsimikiza mtima kuti Yehova amutsogolera komanso amuteteza (Eza 8:21-23 it-1 1158 ¶4)

Nzeru yochokera kwa Mulungu imene Ezara anasonyeza inachititsa kuti mfumu imupatse maudindo akuluakulu. Mofanana ndi Ezara, khalidwe lathu lingachititse kuti dzina la Yehova lilemekezedwe.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi anthu omwe si a Mboni amandilemekeza chifukwa chakuti ndimatsatira zimene Mulungu amafuna?’