July 17-23
EZARA 9-10
Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kusamvera Kumapweteketsa”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eza 10:44—N’chifukwa chiyani akazi ndi ana awo anawatumiza kwawo? (w06 1/15 20 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Eza 9:1-9 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito kapepala kakuti Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi? kuti muyambe kukambirana nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 13)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni ku misonkhano yathu, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 11 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kumvera Kumatiteteza (2At 1:8): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi n’chiyani chichitike Aramagedo isanachitike?
Kodi kukhala omvera kumatithandiza bwanji panopa?
Kodi pali kugwirizana kotani pakati pa Aramagedo ndi kumvera?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 50 mfundo 6-7, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero