Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusamvera Kumapweteketsa

Kusamvera Kumapweteketsa

Aisiraeli ena anakwatirana ndi anthu amene ankalambira mafano (Eza 9:1, 2; w06 1/15 20 ¶1)

Iwo sanatsatire malamulo a Mulungu omwe anali omveka bwino (Eza 9:10-12)

Kusamvera kwawo kunabweretsa mavuto ambiri kwa iwowo komanso mabanja awo (Eza 10:10, 11, 44)

Lamulo lililonse limene Yehova amatipatsa, limakhala lotithandiza. (w09 10/1 10 ¶6) Kumvera kumatithandiza kuti tipewe mavuto ambiri panopa, komanso tidzapeza madalitso osatha m’tsogolo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi kumvera Yehova kwandithandiza bwanji kuti ndipewe mavuto?’