Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

July 3-9

EZARA 4-6

July 3-9

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Musakalowerere Ntchito Yomanga”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Eza 6:13​—N’chifukwa chiyani mawu akuti “kutsidya lina la Mtsinje” ali ochititsa chidwi? (w93 6/15 32 ¶3-5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Eza 4:8-24 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Kuvutika​—Yak 1:13. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU