Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

July 31–August 6

NEHEMIYA 3-4

July 31–August 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Kambiranani tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo m’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)

  • Nkhani: (5 min.) km 11/12 1​—Mutu: Muzisangalala Chifukwa Chogwira Ntchito Mwakhama. (th phunziro 10)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 91

  • Kugwira Ntchito ndi a Mboni za Yehova: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera kuti, Mogwirizana ndi zomwe mwaona muvidiyoyi, kodi khalidwe lathu pa malo ogwirira ntchito lingathandize bwanji anthu kukhala ndi maganizo oyenera okhudza a Mboni?

  • Zofunika Pampingo: (7 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 52

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero