Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?

Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?

Mkulu wa ansembe ndi abale ake sanadzione kukhala anthu apamwamba kwambiri ndipo anagwira nawo ntchito yomanganso mpanda wa Yerusalemu (Ne 3:1)

Anthu ena otchuka “sanagonjere” kuti agwire nawo ntchitoyo (Ne 3:5; w06 2/1 10 ¶1)

Akazi okhulupirika anagwira nawo ntchitoyi yomwe inali yovuta komanso yofuna mphamvu zambiri (Ne 3:12; w19.10 23 ¶11)

Ntchito zambiri zimene zimachitika pampingo, zimafuna mphamvu kapena zimakhala zonyozeka komanso zina ena sangatione tikuzigwira.​—w04 8/1 18 ¶16.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimamva bwanji ndikamagwira ntchito zoterezi, zomwe zimathandiza pa ntchito ya uthenga wabwino?’​—1Ak 9:23.