Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

August 12-18

MASALIMO 73-74

August 12-18

Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Kodi Ndimachitira Nsanje Anthu Amene Satumikira Mulungu?

(10 min.)

Tikhoza kuyamba kuchitira nsanje anthu amene satumikira Yehova (Sl 73:3-5; w20.12 19 ¶14)

Tikamalambira Yehova limodzi ndi abale ndi alongo athu m’malo modzipatula, tikhoza kuyamba kuwaona bwino anthu amene satumikira Mulungu (Sl 73:17; Miy 18:1; w20.12 19 ¶15-16)

Anthu omwe satumikira Mulungu ali “pamalo oterera”; pomwe amene amamutumikira amawapatsa “ulemerero” (Sl 73:18, 19, 24; w14 4/15 4 ¶5; w13 2/15 25-26 ¶3-5)

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 74:13, 14—Kodi mawu akuti “Leviyatani” amanena za chiyani? (it-2 240)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pezani mwayi woti muuze mnzanu zimene mwaphunzira pa misonkhano yampingo yaposachedwapa. (lmd phunziro 2 mfundo 4)

5. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo ndipo musonyezeni mmene phunziro limachitikira. (lmd phunziro 8 mfundo 3)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira

(5 min.) Nkhani. ijwbq 89​—Mutu: Kodi Zipembedzo Zonse N’zabwino? (th phunziro 14)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 72

7. Zofunika Pampingo

(15 min.)

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero