Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

July 1-7

MASALIMO 57-59

July 1-7

Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mfumu Sauli ndi asilikali ake atalephera kugwira Davide

1. Yehova Amasokoneza Anthu Amene Amatsutsa Atumiki Ake

(10 min.)

Davide anakakamizika kuthawa Mfumu Sauli (1Sa 24:3; Sl 57, kamutu)

Yehova anasokoneza zochita za anthu amene ankatsutsa Davide (1Sa 24:7-10, 17-22; Sl 57:3)

Nthawi zina, zimene anthu otsutsa amafuna kuchita zimalephereka (Sl 57:6; bt 220-221 ¶14-15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimadalira Yehova ndikamatsutsidwa?’—Sl 57:2.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 57:7—Kodi kutsimikiza mtima kumatanthauza chiyani? (w23.07 18-19 ¶16-17)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kuchita Khama—Zomwe Paulo Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 7 mfundo 1-2.

5. Kuchita Khama—Zomwe Mungachite Potsanzira Paulo

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 7 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 65

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 78 ndi Pemphero