Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

July 8-14

MASALIMO 60-62

July 8-14

Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Yehova Amatiteteza

(10 min.)

Yehova ali ngati nsanja yolimba (Sl 61:3; it-2 1118 ¶7)

Yehova amatilola kuti tikhale alendo mutenti yake (Sl 61:4; it-2 1084 ¶8)

Yehova ali ngati thanthwe (Sl 62:2; w02 4/15 16 ¶14)


DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi moyo wanga wasintha bwanji chifukwa chakuti ndinadziwa Yehova komanso ndimamudalira?’

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 62:11—Kodi “mphamvu ndi za Mulungu” m’njira yotani? (w06 6/1 11 ¶8)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Yambani kukambirana ndi munthu amene wakusonyezani kukoma mtima. (lmd phunziro 2 mfundo 3)

5. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Muuzeni za JW Library® ndipo musonyezeni mmene angaiikire muchipangizo chake. (lmd phunziro 7 mfundo 4)

6. Nkhani

(5 min.) w22.02 4-5 ¶7-10—Mutu: Muzikhulupirira Yehova Mukapatsidwa Malangizo. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 12

7. Palibe Chimene ‘Chidzatilekanitse ndi Chikondi cha Mulungu’

(10 min.) Nkhani yokambirana.

Onerani VIDIYO. Kenako funsani omvera funso ili:

  • Kodi Yehova anasamalira bwanji M’bale Nyirenda pamene ankazunzidwa?

8. Khalani Bwenzi la Yehova—Zomwe Uyenera Kuchita Kuti Ubatizidwe

(5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO. Kenako ngati n’zotheka itanani ana amene munawasankhiratu kuti abwere papulatifomu ndipo afunseni mafunso awa: Kuti munthu abatizidwe, kodi chofunika kwambiri ndi zaka zake? Fotokozani. Kodi munthu ayenera kuchita zinthu ziti kuti abatizidwe?

9. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero