NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU June 2016
Zitsanzo za Ulaliki
Mfundo zokuthandizani pogawira Galamukani! ndi timapepala. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mupange ulaliki wanuwanu
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Khulupirira Yehova Ndipo Chita Zabwino
Muzigwiritsa ntchito malangizo othandiza a mu Salimo 37.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kuwonjezera Luso Lathu Mu Utumiki—Kugwiritsa Ntchito Mavidiyo Pophunzitsa
N’chifukwa chiyani tiyenera kugwiritsa ntchito mavidiyowa mu utumiki? Nanga angatithandize bwanji kuwonjezera luso lophunzitsa?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yehova Amasamalira Anthu Omwe Akudwala
Mawu a Davide opezeka mu Salimo 41 akhoza kulimbikitsa atumiki okhulupirika amene akudwala kapenanso amene akukumana ndi mavuto enaake?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yehova Sadzasiya Anthu Amtima Wosweka
Mu Salimo 51, Davide akufotokoza mmene tchimo lake linamukhudzira. N’chiyani chinamuthandiza kuti alape?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe
Gwiritsani ntchito mafunso pokambirana zomwe Ufumu wa Mulungu wakwanitsa kuyambira 1914.
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Umutulire Yehova Nkhawa Zako”
Mawu amene Davide analemba pa Salimo 55:22 angatithandize tikakumana ndi vuto lina lililonse.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”
Davide anatamanda Yehova chifukwa cha Mawu ake. Kodi ndi mavesi ati amene anakuthandizani mutakumana ndi mavuto?