June 20-26
MASALIMO 45-51
Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Sadzasiya Anthu Amtima Wosweka”: (10 min.)
Sal. 51:1-4—Davide anadzimvera chisoni kwambiri chifukwa chochimwira Yehova (w93 3/15 10-11 ndime 9-13)
Sal. 51:7-9—Davide ankafuna kuti Yehova amukhululukire kuti ayambirenso kukhala mosangalala (w93 3/15 12-13 ndime 18-20)
Sal. 51:10-17—Davide ankadziwa kuti Yehova amakhululukira munthu ngati walapa mochokera pansi pamtima (w15 6/15 14 ndime 6; w93 3/15 14-17 ndime 4-16)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Sal. 45:4—Kodi ndi mfundo yofunika kwambiri iti ya choonadi yomwe ikufunika kutetezedwa? (w14 2/15 5 ndime 11)
Sal. 48:12, 13—Kodi mavesiwa akutipatsa udindo wotani? (w15 7/15 9 ndime 13)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 49:10–50:6
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g16.3 10-11
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g16.3 10-11
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 3 ndime 1—Pomaliza onetsani vidiyo ya pa jw.org yakuti, Kodi Mlembi Wamkulu wa Baibulo Ndani?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 98
“Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe”: (15 min.) Mafunso ndi mayankho. Yambani ndi kuonetsa vidiyo ya pa jw.org yakuti, Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe mpaka pachigawo chakuti, “Ankaphunzira Zinthu Zozama kwa Tsiku Limodzi Lokha.” (Pitani pamene palembedwa kuti, MABUKU > MAVIDIYO.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia tsamba 2-3 ndi mawu oyamba ndime 1-15
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 109 ndi Pemphero