June 13-19
MASALIMO 38-44
Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amasamalira Anthu Omwe Akudwala”: (10 min.)
Sal. 41:1, 2—Wodala ndi munthu amene amaganizira anthu onyozeka (w15 12/15 24 ndime 7; w91 10/1 14 ndime 6)
Sal. 41:3—Yehova amasamalira owongoka mtima pamene akudwala (w08 9/15 5 ndime 12-13)
Sal. 41:12—Kudziwa kuti matenda adzatha kungathandize anthu omwe akudwala kuti apirire (w15 12/15 27 ndime 18-19; w08 12/15 6 ndime 15)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Sal. 39:1, 2—Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tizikhala osamala poyankhula? (w09 5/15 4 ndime 6; w06 5/15 20 ndime 11)
Sal. 41:9—Kodi Yesu anasonyeza bwanji kuti zimene zinachitikira Davide zidzachitikiranso iyeyo? (w11 8/15 13 ndime 5; w08 9/15 5 ndime 11)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 42:6–43:5
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Tsamba loyamba la g16.3
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Tsamba loyamba la g16.3
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 2 ndime 4-5—Pomaliza fotokozerani munthuyo zokhudza vidiyo yakuti Kodi Mulungu Ali ndi Dzina?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 128
Yang’ananibe Pamphoto!: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Khalani Bwenzi la Yehova—Yang’ananibe Pamphoto (Nyimbo Na. 24). (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Kenako kambiranani mbali yakuti “Kuyerekezera: Moyo Wapanopa ndi Wam’tsogolo,” pogwiritsa ntchito mafunso otsatirawa: Kodi ndi zinthu ziti zomwe zidzasinthe m’Paradaiso? Kodi ndi zinthu zabwino ziti zimene mukuyembekezera? Kodi kuganizira zimene mukuyembekezera m’tsogolo kungakuthandizeni bwanji kuti mupirire?—2 Akor. 4:18.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) cl mutu 31 ndime 21-23, ndi bokosi patsamba 319
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero