Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

June 4-10

MALIKO 15-16

June 4-10

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesu Anakwaniritsa Maulosi”: (10 min.)

    • Maliko 15:3-5​—Pamene ankaimbidwa mlandu, Yesu sanayankhe chilichonse

    • Maliko 15:24, 29, 30​—Anthu anachita maere pazovala zake ndipo ankamunyoza komanso kumuseka (“kugawana malaya ake akunja” “kupukusa mitu yawo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 15:24, 29, nwtsty)

    • Maliko 15:43, 46​—Anaikidwa m’manda a anthu olemera (“Yosefe” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 15:43, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 15:25​—N’chifukwa chiyani pali kusiyana pa nkhani ya nthawi yomwe Yesu anapachikidwa? (“cha m’ma 9 koloko m’mawa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 15:25, nwtsty)

    • Maliko 16:8​—N’chifukwa chiyani mu Uthenga Wabwino wa Maliko, mu Baibulo la Dziko Latsopano lokonzedwanso lachingelezi, mulibe mawu omaliza aatali komanso aafupi? (“anagwidwa ndi mantha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 16:8, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 15:1-15

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU