NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU June 2019
Zimene Tinganene
Zitsanzo za ulaliki zofotokoza nkhani zokhudza mmene moyo udzakhalire masiku otsiriza akadzatha.
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Nkhani ‘Yophiphiritsira’ Yomwe ndi Yofunika Kwambiri kwa Ife
Kodi Sara, mkazi wa Abulahamu, komanso Hagara ankaimira chiyani?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Zimene Ulamuliro wa Yehova Ukuchita
Kodi ulamuliro wa Yehova n’chiyani nanga tingasonyeze bwanji kuti tili kumbali yake?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Muzipindula Mokwanira Mukamaphunzira Panokha
Kodi ndi zinthu ziti zomwe zingatithandize kuti tizipindula mokwanira tikamaphunzira Baibulo patokha?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Valani Zida Zonse Zankhondo Zochokera kwa Mulungu”
Akhristu ali ngati asilikali. Tchulani dzina la chida chilichonse komanso zimene chikutanthauza.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kodi Maganizo a Yehova Ndi Otani pa Nkhaniyi?
Kodi tingazindikire bwanji chifuniro cha Yehova n’kumachita zimene amafuna?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Musamade Nkhawa ndi Kanthu Kalikonse”
Zinthu zodetsa nkhawa zikuchuluka masiku ano. Kodi tingatani kuti tisamade nkhawa kwambiri?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kodi Mumasankha Zosangalatsa Mwanzeru?
Kodi tingatani kuti tizisangalatsa Mulungu tikamachita zinthu zosangalatsa?