June 10-16
AEFESO 1-3
Nyimbo Na. 112 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Ulamuliro wa Yehova Ukuchita”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Aefeso.]
Aef. 1:8, 9—“Chinsinsi chopatulika” ndi chokhudza Ufumu wa Mesiya (it-2 837 ¶4)
Aef. 1:10—Yehova akugwirizanitsa anthu komanso angelo (w12 7/15 27-28 ¶3-4)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aef. 3:13—Kodi masautso a Paulo ‘ankatanthauza ulemerero’ kwa Aefeso m’njira yotani? (w13 2/15 28 ¶15)
Aef. 3:19—Kodi timadziwa bwanji “chikondi cha Khristu”? (cl 299 ¶21)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aef. 1:1-14 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 3)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musonyezeni chimodzi mwa zinthu zimene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzipindula Mokwanira Mukamaphunzira Panokha”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Pitirizani “Kugwira Mwamphamvu Mawu a Moyo” Pophunzira Mwakhama.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 39
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 120 ndi Pemphero