June 17-23
AEFESO 4-6
Nyimbo Na. 71 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Valani Zida Zonse Zankhondo Zochokera kwa Mulungu”: (10 min.)
Aef. 6:11-13—Timafunika kutetezedwa kuti Satana ndi ziwanda zake asatigonjetse (w18.05 27 ¶1)
Aef. 6:14, 15—Muzidziteteza ndi choonadi, chilungamo komanso uthenga wabwino wamtendere (w18.05 28-29 ¶4, 7, 10)
Aef. 6:16, 17—Muzidziteteza ndi chikhulupiriro, chiyembekezo cha chipulumutso komanso Mawu a Mulungu (w18.05 29-31 ¶13, 16, 20)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aef. 4:30—Kodi munthu angamvetse bwanji chisoni mzimu woyera wa Mulungu? (it-1 1128 ¶3)
Aef. 5:5—Kodi munthu waumbombo amakhala bwanji wopembedza mafano? (it-1 1006 ¶2)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aef. 4:17-32 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulaliki. Musonyezeni ndi kukambirana mfundo za m’vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (koma musaonetse vidiyoyi) (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Maganizo a Yehova Ndi Otani pa Nkhaniyi?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Pitirizani Kuzindikira Chifuniro cha Yehova (Lev. 19:18).
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 40
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero