June 3-9
AGALATIYA 4-6
Nyimbo Na. 16 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nkhani ‘Yophiphiritsira’ Yomwe ndi Yofunika Kwambiri kwa Ife”: (10 min.)
Agal. 4:24, 25—Hagara ankaimira mtundu wa Isiraeli womwe unkatsatira Chilamulo (it-1 1018 ¶2)
Agal. 4:26, 27—Sara ankaimira “Yerusalemu wam’mwamba,” yemwe ndi mbali yakumwamba ya gulu la Yehova (w14 10/15 10 ¶11)
Agal. 4:28-31—Anthu omvera adzadalitsidwa kudzera mwa “ana” a Yerusalemu wam’mwamba
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Agal. 4:6—Kodi mawu achiheberi kapena achialamu akuti abba, amatanthauza chiyani? (w09 4/1 13)
Agal. 6:17—Kodi n’kutheka kuti mtumwi Paulo ankatanthauza chiyani ponena kuti thupi lake linali ndi “zipsera za chizindikiro cha kapolo wa Yesu?” (w10 11/1 15)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Agal. 4:1-20 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kufotokoza Bwino Malemba, kenako kambiranani phunziro 6 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w12 3/15 30-31—Mutu: N’chifukwa Chiyani Akhristu Ayenera Kupeweratu Kuwonera Zolaula? (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (8 min.)
Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 38
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 147 ndi Pemphero