NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU June 2020
Zimene Tinganene
Zitsanzo za zimene tinganene zokhudza masiku otsiriza a dziko loipali.
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yosefe Anakhululukira Azichimwene Ake
Kodi tingaphunzire chiyani pa chitsanzo cha Yosefe pa nkhani yokhululukira ena?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Chakudya pa Nthawi ya Njala
Ngakhale kuti m’dzikoli muli njala yauzimu, kodi n’kuti kumene tingapeze chakudya chauzimu chochuluka?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Achikulire Angatiphunzitse Zambiri
Kodi ndi motani mmene achikulire alili zitsanzo zabwino pa nkhani yokhala ndi chikhulupiriro?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zimene Tingaphunzire kwa Akhristu Omwe Atumikira kwa Nthawi Yaitali
Kodi tingatani kuti tipindule ndi zimene Akhristu omwe atumikira Yehova kwa zaka zambiri akhala akukumana nazo?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”
Kodi tanthauzo la dzina la Mulungu limakukhudzani bwanji?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ine Ndidzakhala Nawe Polankhula”
Kodi chitsanzo cha Mose chingatithandize bwanji kuti tisamaope tikamagwira ntchito yolalikira?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Mmene Tingagwiritsire Ntchito Zitsanzo za Zimene Tinganene
Kodi mungagwiritse ntchito bwanji zitsanzo za zimene tinganene zomwe zimapezeka mu utumiki komanso moyo wathu wachikhristu mukamakamba nkhani za ophunzira komanso mukakhala mu utumiki?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Mungathe Kulalikira Komanso Kuphunzitsa
Kodi chingakuthandizeni n’chiyani kuti mupeze mphamvu komanso kuti mukhale olimba mtima mukamalalikira ndiponso kuphunzitsa?