June 1-7
GENESIS 44-45
Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yosefe Anakhululukira Azichimwene Ake”: (10 min.)
Gen. 44:1, 2—Yosefe anayesa azichimwene ake kuti aone ngati anali atasintha (w15 5/1 14-15)
Gen. 44:33, 34—Yuda anapempha Yosefe kuti amasule Benjamini
Gen. 45:4, 5—Yosefe anatsanzira Yehova pa nkhani yokhululuka
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Gen. 44:13—Kodi kung’amba zovala kunkatanthauza chiyani? (it-2 813)
Gen. 45:5-8—N’chiyani chingatithandize kupirira anthu ena akatichitira zopanda chilungamo? (w04 8/15 15 ¶15)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Gen. 45:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Nkhani Yophunzitsadi Anthu, kenako kambiranani phunziro 18 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w06 2/1 31—Mutu: Kodi Yosefe anagwiritsa ntchito kapu yapadera yasiliva poombeza maula, monga mmene lemba la Genesis 44:5, 15 limamvekera? (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 86 ndime 8-17
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero