June 29–July 5
EKISODO 4-5
Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ine Ndidzakhala Nawe Polankhula”: (10 min.)
Eks. 4:10, 13—Mose ankadziona kuti sangakwanitse utumiki umene anapatsidwa (w10 10/15 13-14)
Eks. 4:11, 12—Yehova anamutsimikizira kuti adzamuthandiza (w14 4/15 9 ¶5-6)
Eks. 4:14, 15—Yehova anauza Mose kuti Aroni adzamuthandiza (w10 10/15 14)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks. 4:24-26—N’chifukwa chiyani Zipora ananena kuti Yehova ndi “mkwati wa magazi”? (w04 3/15 28 ¶4)
Eks. 5:2—Kodi Farao ankatanthauza chiyani ponena kuti sankamudziwa Yehova? (it-2 12 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks. 4:1-17 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 2)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 4)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 100 ¶15-16 (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mmene Tingagwiritsire Ntchito Zitsanzo za Zimene Tinganene”: (5 min.) Nkhani yokambirana.
“Mungathe Kulalikira Komanso Kuphunzitsa”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Molimba Mtima—Ofalitsa.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 89
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero