Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 8-11

Anthu Akamatsogoleredwa ndi Yehova Zinthu Zimawayendera Bwino

Anthu Akamatsogoleredwa ndi Yehova Zinthu Zimawayendera Bwino

Anthu alibe luso komanso ufulu woti azidzilamulira okha

10:21-23

  • Aisiraeli anabalalika chifukwa choti abusa awo sankafunafuna Yehova

  • Anthu amene ankatsatira malangizo a Yehova anali pa mtendere, ankakhala mosangalala komanso zinthu zinkawayendera bwino