Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mapeto a Dziko Loipali Ali Pafupi Kwambiri

Mapeto a Dziko Loipali Ali Pafupi Kwambiri

Onerani vidiyo yakuti, Mapeto a Dziko Loipali Ali Pafupi Kwambiri, ndipo kenako kambiranani mafunso otsatirawa omwe ndi okhudza lemba la Mateyu 24:34.

  • Kodi “zinthu zonsezi” zomwe zatchulidwa palembali ndi chiyani?

  • Kodi lemba la Ekisodo 1:6 limatithandiza bwanji kumvetsa tanthauzo la mawu akuti “m’badwo”?

  • Kodi Yesu ankanena za m’badwo uti kwenikweni?

  • Kodi ndi magulu awiri ati amene apanga “m’badwo uwu”?

  • Kodi mawu a Yesu akusonyeza bwanji kuti tikukhala m’nthawi yamapeto yeniyeni?