Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 24

Pitirizani Kukhala Maso M’masiku Otsiriza Ano

Pitirizani Kukhala Maso M’masiku Otsiriza Ano

24:39

Anthu ambiri masiku ano amalola kuti zinthu zatsiku ndi tsiku ziwalepheretse kuchita zinthu zokhudza kulambira. Kodi Akhristu olimba mwauzimu amasiyana bwanji ndi anthu a m’dzikoli pa nkhani ya mmene amaonera . . .

  • maphunziro apamwamba?

  • zosangalatsa?

  • ntchito?

  • chuma?