March 11-17
AROMA 15-16
Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzidalira Yehova Kuti Akulimbikitseni Komanso Kukuthandizani Kupirira”: (10 min.)
Aroma 15:4—Muziwerenga Mawu a Mulungu kuti azikulimbikitsani (w17.07 14 ¶11)
Aroma 15:5—Muzipempha Yehova kuti akuthandizeni kukhala opirira komanso kuti akutonthozeni (w16.04 14 ¶5)
Aroma 15:13—Yehova amatipatsa chiyembekezo (w14 6/15 14 ¶11)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aroma 15:27—Kodi anthu a mitundu ina omwe anadzakhala Akhristu “anali ndi ngongole” kwa Akhristu a ku Yerusalemu m’njira yotani? (w89 12/1 24 ¶3)
Aroma 16:25—Kodi “chinsinsi chopatulika chimene chakhala chobisika kuyambira nthawi zakale” n’chiyani? (it-1 858 ¶5)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 15:1-16 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 3)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 10)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Yehova ‘Amatonthoza Komanso Amapereka Mphamvu’: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:
Kodi Yehova amatilimbikitsa bwanji?
Kodi mwaphunzira zotani pa nkhani yolimbikitsa ena?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 29
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 146 ndi Pemphero