Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 15-16

Muzidalira Yehova Kuti Akulimbikitseni Komanso Kukuthandizani Kupirira

Muzidalira Yehova Kuti Akulimbikitseni Komanso Kukuthandizani Kupirira

15:4-7

Njira imodzi imene Yehova amatilimbikitsira komanso kutithandiza kupirira ndi kudzera m’Mawu ake. Kodi nkhani za m’Baibulo za anthu otsatirawa zingakulimbikitseni bwanji, nanga zingakuthandizeni bwanji kupirira?

  • Nowa

  • Yosefe

  • Davide