March 25-31
1 AKORINTO 4-6
Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chofufumitsa Chaching’ono Chimafufumitsa Mtanda Wonse”: (10 min.)
1 Akor. 5:1, 2—Mpingo wa ku Korinto unkalekerera munthu wina yemwe ankachita zoipa
1 Akor. 5:5-8, 13—Paulo anauza akulu kuti achotse “chofufumitsa” popereka munthuyo kwa Satana (it-2 230, 869-870)
1 Akor. 5:9-11—Anthu a mumpingo sayenera kumachezabe ndi munthu yemwe sakufuna kulapa (lvs 241, Mawu Akumapeto “Kuchotsa Munthu Mumpingo”)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
1 Akor. 4:9—Kodi atumiki a Mulungu a padziko lapansi amakhala bwanji ngati “choonetsedwa m’bwalo la masewera” kwa angelo? (w09 5/15 24 ¶16)
1 Akor. 6:3—Kodi Paulo ankatanthauza chiyani pamene analemba kuti: “Tidzaweruza angelo”? (it-2 211)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Akor. 6:1-14 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 11)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) lvs 44 (th phunziro 3)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzigwiritsa Ntchito Mavidiyo Pophunzira ndi Anthu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani ndi kukambirana vidiyo yosonyeza wofalitsa akugwiritsa ntchito vidiyo ya phunziro 4 m’kabuku ka Uthenga Wabwino.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 31
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 139 ndi Pemphero