March 4-10
AROMA 12-14
Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mmene Tingasonyezere Chikondi Chachikhristu”: (10 min.)
Aroma 12:10—Muzikonda Akhristu anzanu (it-1 55)
Aroma 12:17-19—Munthu akakulakwirani, musamabwezere (w09 10/15 8 ¶3; w07 7/1 24-25 ¶12-13)
Aroma 12:20, 21—Gonjetsani choipa pochita chabwino (w12 11/15 29 ¶13)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aroma 12:1—Kodi vesi limeneli likutanthauza chiyani? (lvs 76-77 ¶5-6)
Aroma 13:1—Kodi “olamulira amene alipowa ali m’malo awo osiyanasiyana mololedwa ndi Mulungu” m’njira yotani? (w08 6/15 31 ¶4)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 13:1-14 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kugwiritsa Ntchito Mafunso, kenako kambiranani phunziro 3 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w11 9/1 21-22—Mutu: N’chifukwa Chiyani Akhristu Amafunikabe Kulipira Misonkho Ngakhale Kuti Ndalamazo Zingagwiritsidwe Ntchito pa Zinthu Zosagwirizana ndi Malemba? (th phunziro 3)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 28, ndi bokosi lakuti “Mafanizo Onena za Kusala Kudya”
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero