Abulahamu anali womvera ndipo anapita ndi Isaki ku Moriya

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU March 2020

Zimene Tinganene

Zitsanzo za zimene tinganene zokhudza Yesu Khristu komanso nsembe imene anapereka.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Mulungu Anayesa Abulahamu’

Kodi n’chifukwa chiyani Yehova anauza Abulahamu kuti apereke mwana wake ngati nsembe?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Isaki Anapeza Mkazi

Kodi tingaphunzire chiyani kwa mtumiki wa Abulahamu tikafuna kusankha zochita pa nkhani zikuluzikulu?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Ndiitane Ndani?

Kodi mukufuna kudzaitana ndani pa mwambo wokumbukira imfa ya Khristu umene ukubwera kutsogoloku?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Esau Anagulitsa Ukulu Wake

Kodi ndi zinthu zopatulika ziti zomwe muyenera kuyamikira?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yakobo Analandira Madalitso

Kodi Yakobo analandira bwanji madalitso ake?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yakobo Anakwatira

Kodi mungatani kuti muzikhalabe osangalala m’banja ngakhale mutakumana ndi mavuto?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzilalikira Anthu Osaona

Kodi tingatengere bwanji chitsanzo cha Yehova tikamathandiza anthu osaona m’gawo lathu?