Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 25-26

Esau Anagulitsa Ukulu Wake

Esau Anagulitsa Ukulu Wake

25:27-34

Esau ‘sanayamikire zinthu zopatulika.’ (Ahe 12:16) Iye anagulitsa ukulu wake ndipo kenako anakwatira akazi awiri achikunja.​—Ge 26:34, 35.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimayamikira zinthu zopatulika zotsatirazi?’

  • Ubwenzi wanga ndi Yehova

  • Mzimu woyera

  • Kudziwika ndi dzina loyera la Yehova

  • Ntchito yolalikira

  • Misonkhano

  • Ukwati