Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 22-23

‘Mulungu Anayesa Abulahamu’

‘Mulungu Anayesa Abulahamu’

22:1, 2, 9-12, 15-18

Abulahamu anamva chisoni kwambiri pamene ankafuna kupereka nsembe mwana wake Isaki. Zimenezi zimatithandiza kumvetsa mmene Yehova anamvera pamene ankapereka mwana wake Yesu Khristu monga dipo. (Yoh 3:16) Kodi mawu amene Yehova ananena muvesi 2 akutithandiza bwanji kudziwa mmene amamvera?

Kodi mumamva bwanji mukaganizira chikondi chimene Yehova ali nacho?​1Ak 6:20; 1Yo 4:11