March 23-29
GENESIS 27-28
Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yakobo Analandira Madalitso”: (10 min.)
Ge 27:6-10—Rabeka anathandiza Yakobo kuti alandire madalitso amene ankayenera kulandira (w04 4/15 11 ¶4-5)
Ge 27:18, 19—Yakobo ananamizira kuti anali Esau pokaonekera kwa bambo ake (w07 10/1 31 ¶2-3)
Ge 27:27-29—Isaki anadalitsa Yakobo ngati mwana wake woyamba kubadwa (it-1 341 ¶6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Ge 27:46–28:2—Kodi anthu apabanja angaphunzire chiyani kwa Isaki ndi Rabeka? (w06 4/15 6 ¶3-4)
Ge 28:12, 13—Kodi loto la Yakobo lokhudza “makwerero” likusonyeza chiyani? (w04 1/15 28 ¶6)
Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ge 27:1-23 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi, kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi wofalitsayu anasonyeza bwanji kuti amamvetsera pamene mwininyumba amafotokoza maganizo ake? Kodi wofalitsayu anagwiritsa ntchito bwanji zinthu zomwe timagwiritsa ntchito pophunzitsa?
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) jl phunziro 17 (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 78
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero