Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 27-28

Yakobo Analandira Madalitso

Yakobo Analandira Madalitso

27:6-10, 18, 19, 27-29

Madalitso amene Yakobo analandira kuchokera kwa bambo ake, anali ulosi wa zimene zidzachitike m’tsogolo.

  • 27:28​—Yehova anapatsa mbadwa za Yakobo dziko lachonde “loyenda mkaka ndi uchi.”​—De 26:15

  • 27:29​—Aisiraeli (mbadwa za Yakobo) anadzakhala mtundu wamphamvu kuposa Aedomu (mbadwa za Esau).​—Ge 25:23; 2Sa 8:14

  • 27:29​—Aedomu anatembereredwa chifukwa ankadana ndi Aisiraeli ndipo patapita nthawi anawonongedwa.​—Eze 25:12-14