Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 24

Isaki Anapeza Mkazi

Isaki Anapeza Mkazi

24:2-4, 11-15, 58, 67

Mtumiki wa Abulahamu anapempha Yehova kuti amuthandize kusankha mkazi wa Isaki. (Ge 24:42-44) Nafenso tizipempha Yehova kuti atithandize kusankha zoyenera kuchita pa nkhani zikuluzikulu. Kodi tingachite bwanji zimenezi?

  • Tizipemphera

  • Tiziwerenga Mawu a Mulungu komanso tizifufuza m’mabuku athu

  • Tizipempha abale ndi alongo olimba mwauzimu kuti atithandize nzeru