April 19-25
NUMERI 22-24
Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Nu 22:20-22—N’chifukwa chiyani Yehova anakwiyira kwambiri Balamu? (w04 8/1 27 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 23:11-26 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu.
Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 5 ¶3-4 (th phunziro 6)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Amasintha Chizunzo N’kukhala Mwayi Wolalikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kucheza ndi Dmitriy Mikhaylov.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 130
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 15 ndi Pemphero