MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Yehova Amasintha Chizunzo N’kukhala Mwayi Wolalikira
Nthawi zambiri cholinga cha anthu amene amatizunza chimakhala kulepheretsa ntchito yolalikira. Koma tikakhalabe wokhulupirika pamene tikuzunzidwa, Yehova amalemekezedwa.
ONERANI VIDIYO YAKUTI KUCHEZA NDI DMITRIY MIKHAYLOV NDIPO KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:
-
Kodi M’bale Mikhaylov anakumana ndi mavuto otani?
-
Kodi Yehova anathandiza bwanji M’bale Mikhaylov kupirira?
-
Kodi Yehova anagwiritsa ntchito bwanji chizunzo chimene M’bale Mikhaylov anakumana nacho kuti akaidi ena amve uthenga wabwino?