Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso

Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso

Amowabu ankafuna kuchitira zoipa Aisiraeli (Nu 22:3-6)

Yehova anathandiza anthu ake (Nu 22:12, 34, 35; 23:11, 12)

Palibe amene angalimbane ndi Yehova (Nu 24:12, 13; bt 53 ¶5; it-2 291)

Vuto lililonse, ngakhalenso chizunzo, silingalepheretse kuti uthenga wabwino ulalikidwe mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu. Tikakumana ndi mavuto, kodi timadalira Atate wathu wakumwamba n’kumaonabe kuti kumulambira ndiye kofunika kwambiri?