April 26–May 2
NUMERI 25-26
Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Nu 26:55, 56—Kodi mmene Yehova anagawira cholowa cha malo ku mafuko a Aisiraeli zinasonyeza bwanji kuti ndi wanzeru? (it-1 359 ¶1-2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 25:1-18 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo ndipo kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyo. (th phunziro 3)
Nkhani (5 min.) w04 4/1 29—Mutu: N’chifukwa Chiyani Chiwerengero Chomwe Chili pa Numeri 25:9 Chimasiyana ndi cha pa 1 Akorinto 10:8? (th phunziro 17)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzisankha Anzanu Mwanzeru”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani mbali ya vidiyo yakuti Zitsanzo Zotichenjeza Masiku Ano.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 131
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 145 ndi Pemphero