April 5-11
NUMERI 17-19
Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ine Ndine . . . Cholowa Chako”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Nu 18:19; mawu a m’munsi.—Kodi mawu akuti “pangano losatha la mchere” akutanthauza chiyani? (g02 6/8 14 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 18:1-13 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Yesu—Mt 20:28. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Musonyezeni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)
Nkhani: (5 min.) w18.01 18 ¶4-6—Mutu: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupereka kwa Yehova? (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 128
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero