Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

March 1-7

NUMERI 7–8

March 1-7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Itanirani ku Chikumbutso munthu amene munkaphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Itanirani ku Chikumbutso wachibale amene munamulalikirapo m’mbuyomu. (th phunziro 17)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU