Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli

Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli

Amuna audindo amatsogolera pa utumiki wopatulika (Nu 7:10; it-1 497 ¶3)

Atumiki a Mulungu ayenera kuchita zinthu mwadongosolo (Nu 7:11; it-2 796 ¶1)

Yehova amadziwa kuti atumiki ake ena sangakwanitse kuchita zinthu zina (Nu 8:25, 26; w04 8/1 25 ¶1)

Mofanana ndi mmene ankachitira ndi Aisiraeli, masiku anonso Yehova amathandiza anthu ake kuchita zinthu mwadongosolo monga gulu. Komabe iye amaona mtumiki wake aliyense komanso khama limene amachita pomutumikira.