Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Chikhulupiriro Chimatithandizira Kukhala Olimba Mtima

Mmene Chikhulupiriro Chimatithandizira Kukhala Olimba Mtima

Azondi amene anapereka lipoti labodza analibe chikhulupiriro (Nu 13:31-33; 14:11)

Kupanda chikhulupiriro kwa azondi 10 kunafooketsa abale awo (Nu 14:1-4)

Azondi amene anapitiriza kukhala olimba mtima anali ndi chikhulupiriro cholimba (Nu 14:6-9; w06 10/1 17 ¶5-6)

Aisiraeli anali ataona kale mmene Yehova anawapulumutsira m’mbuyomo. Zimenezi zinkayenera kulimbitsa chikhulupiriro chawo kuti awathandiza kugonjetsa Akanani.